Welcome to Malaw Lero! Dive into the pulse of Malawi with our channel, where we bring you the latest trends, hot topics, and vibrant stories from across the country. Whether it’s breaking news, cultural highlights, or exciting local events, we cover it all with insightful commentary and up-to-date information. Subscribe and stay informed about what’s trending in Malawi today!
Malawi Lero
#TheDailyTimes front page: The main opposition Malawi Congress Party (MCP) yesterday punched holes in the mid-year national budget presented by Finance Minister Joseph Mwanamvekha on Friday, describing it as a demonstration of what they described as lack of faithfulness and truthfulness.
6 months ago | [YT] | 7
View 0 replies
Malawi Lero
ZOTSATIRA ZA KAFUKUFUKU WA #IPORSURVEYFINDINGS WAONETSA KUTI.
Amalawi 41 pa 100 alionse ati ali ndi malingaliro odzavotera a Peter Mutharika a chipani cha DPP, pomwe 31 pa 100 akuti adzasankha mtsogoleri wa MCP a Lazarus Chakwera ndipo ena 6 pa 100 alionse asankha a Dalitso Kabambe a chipani cha UTM.
Izi ndi malingana ndi kafukufuku wa bungwe la Institute of Public Opinion and Research omwe waonetsanso kuti anthu atatu pa 100 asankha kudzavotera a Atupele Muluzi a UDF awiri asankha a Joyce Banda.
Bungweli latsindika kuti izi sizikulosefa mmene zidzakhalire pa chisankho cha chaka chino, koma zikungoonetsera mmene anthu akufunira pakadali pano, ndipo lapempha mbali zosiyanasiyana kugwirana manja polimbikitsa anthu kuti adzatuluke kukavota.
SOURCE :Times 360
Wolemba Daniel Zimba
Dziwaninso kuti uku sikukhala kulosera koma kupenekera malinga ndi zomwe anthu akukamba.
8 months ago | [YT] | 86
View 17 replies
Malawi Lero
MPIRA WADZULO UNAKOMATU👇
https://youtu.be/-Xm1jz8ftZY
11 months ago | [YT] | 2
View 0 replies
Malawi Lero
Black box yapezeka ku India!
11 months ago | [YT] | 16
View 0 replies
Malawi Lero
#Times360Malawi
#MzDemos
Mavenda ena anabweretsa bokosi loti anyamule pa ziwonetsero zawo koma apolisi aliphwasulula.
Bokosi analikuta ndi nsalu ya chipani cha MCP.
Pakadali pano ziwonetsero sizidayambebe chifukwa mavendawa akudikira chimkuzamawu.
Galimoto zokwana khumi ndi imodzi za apolisi ndizomwe zafika pa malo omwe ziwonetsero ziyambe pa msika wa Zigwagwa.
Olemba ndikujambula: Sam Kalimira
1 year ago | [YT] | 4
View 1 reply
Malawi Lero
Sad:
Pope Francis dies at the age of 88. Vatican confirmed..
1 year ago | [YT] | 7
View 0 replies
Malawi Lero
@MalawiLero
Woyimba wodziwika bwino, Skeffa Chimoto, lero wapambana chisankho cha chipulura m'dera la Nkhotakota-Nkhula m’boma la Nkhotakota.
A Chimoto apambana ndi mavoti 934 kugonjetsa a Gerald Makokola omwe apeza mavoti 405 ndi a Osman Mkanyila Saidi omwe apeza mavoti 10.
Chisankhochi chachitika lero kutsatira kuimitsidwa kwa chisankho choyamba chomwe chinachitika m'derali mwezi wa February kamba ka zotsamwitsa zina zomwe akuluakulu a chipani cha MCP anazipeza pa nthawiyo.
Izi zikutanthauza kuti a Chimoto ndi omwe adzaimire ngati phungu wa nyumba ya malamulo m'derali pa chisankho cha pa 16 September.
1 year ago | [YT] | 8
View 6 replies
Malawi Lero
Zikafika apa mumatani?
1 year ago | [YT] | 14
View 3 replies
Malawi Lero
Membala wa MCP komanso wothandizira, Lovemore Chauwa wasumira pulezidenti wa chipanichi Dr Lazarus Chakwera ndi utsogoleri wa MCP chifukwa chochita zisankho zachipani pogwiritsa ntchito mamembala osavomerezeka omwe udindo wawo wotsatira malamulo udatha kalekale.
#MALAWILERO
#mbiri
1 year ago | [YT] | 4
View 4 replies
Malawi Lero
Gerald chavez Kampanikiza writes :
Ukakhara kuti ukuyembekezera kwambiri kuposa aliyese kuti Dr Laz azatenga iwe ngati running mate umawopatu aliyese okumana ndi President mkuyamba kumubaya. Ndikunena pano ayamba kale kunjenjemera mantha awagwira, inu president amakumana ndi munthu wina aliyese chonde ndipo aka sikoyamba kukumana ndi AAM.
1 year ago | [YT] | 6
View 5 replies
Load more